Imagine you go to church. You know it is time for the Psalm, but in the bulletin you see the heading: Salimo 1. Under it, you try to solve the new puzzle of a new language.
Ngwodala munthu wosatsata uphungu wa anthu oipa,
wosatsanzira mayendedwe a anthu ochimwa,
wosakhala nawo m’gulu la anthu onyoza Mulungu,
koma wokondwerera kumvera malamulo a Chauta,
nkumasinkhasinkha za malamulowo usana ndi usiku.
Munthuyo ali ngati mtengo wobzalidŵa m’mbali mwa mtsinje wa madzi,
ngati mtengo wobereka zipatso pa nthaŵi yake,
umene masamba ake safota konse.
Zochita zake zonse zimamuyendera bwino. Continue reading “Water for Roots and Fruits”